Artist: SevenOmore (MW)
Lyrics of Artist: SevenOmore (MW)
Lyrics of Artist: SevenOmore (MW)
[Lyric] Pogona (SevenOmore (MW))
[Intro] Yah Oh-yah-yah Oh-yah-yah Oh-yah-yah Oh-yah-yah [Chorus] Amandikonda pogona Amandifuna pogona Amandikonda pogona Amandifuna pogona Amandikonda pogona, gona Kunkonda pogona Amandifuna pogona, gona Kunfuna pogona [Verse] Kumbali amandikana, amati ine ndine hule Kumbali amandinyoza, ati ndine osauka Kumbali amandikana, amangoti ndine...Learn MorepopSevenOmore (MW)[Lyric] Zonsezi (SevenOmore (MW))
[Intro] Yah Ya achina Seven adah [Chorus] Ambuye amatikonda (Yah) Mulungu amatikonda (Yah) Chauta amatikonda (Yah) Ambuye amatikonda (Yah) Amatidzutsa tikagwa Amatichilitsa tikadwala Timuyimbile kuti izi-pitilile [Verse 1] Ambuye amakonda aliyense Mphepo imapeza aliyense Mvula imagwera denga la aliyense Dzuwa limapeza aliyense (Yah) Onani munthu,...Learn MorerapSevenOmore (MW)