Song: Zifukwa
Artist:  KIOSK (MW)
Year: 2021
Viewed: 0 - Published at: 10 years ago

[Intro: Starnel Mon]
(Welcome to year 2099)
Aah papalala pala papalala (Tiye, tiye, tiye)
Muli ndi zifukwa
Muli ndi zi--
Ooow (EMB)
Ooh am on my miracle height
(Its Thug Records)

[Verse 1: Starnel Mon]
She thinks that I don't love her (She don't really care)
She say ndimamuganizila nkangolota (Bola chithe)
Nanga pamene paja umatani (Tani)
Nanga unali naye uja ndi ndani (Ndani)
Ndikalakwitsa ndimapanga makani
Usazapiteso ndakupanga Barn
Muli ndi zifukwa sis (Sis)
Chikhala ndi zoona zikanatchuka sis (Sis)
Inu mumangovuta sis
Ndikatelo amakwiya sis (Sis)
Nkhani yake jealous mkazi asandipatse bho (Jealous)
Amene uja ndi ndan (Eva, jealous)
Ndiye mumacheza chani (Ah, jealous, jealous, yea)
[Pre-Chorus: KIOSK]
You cannot come at my house jus to chat can't you come to chill
Mukangot high Ku DM kwanga ndimadziwa kuti

[Chorus: Starnel Mon]
Muli ndi zifukwa (kwa)
Fukwa, fukwa, fukwa
Muli ndi zifukwa (kwa) fukwa, fukwa, fukwa

[Verse 2: KIOSK]
Yea akangot high ndimadziwa kut akufuna cash
I want this and that if you can never do it you don't really love mе
Aaah sukufuna chikondi sundinvetsa mwina ndiwe gonthi
Bwanj umandi treatеr chonchi
Ulibe nthaw yanga ngakhale uli ndi watch
So now know the gist all I ever wished was kuti uzindikonda mene ndilili
Umabwela ndi zifukwa zambili mbili nsayike mkazi pa status you like who is this
So now know the gist all I ever wished was kuti uzindikonda mene ndilili
Umabwela ndi zifukwa zambili mbili
Nsayike mkazi pa status you like who is this, yea

[Pre-Chorus: KIOSK]
You cannot come at my house jus' to chat can't you come to chill
Mukangot high ku DM kwanga ndimadziwa kuti

[Chorus: Starnel Mon]
Muli ndi zifukwa (kwa)
Fukwa, fukwa, fukwa
Muli ndi zifukwa (kwa) fukwa, fukwa, fukwa

( KIOSK (MW) )
www.ChordsAZ.com

TAGS :